06/08/2026
ποΈ NTCHITO YABWINO IKUPITILIRA. NJIRA YA FINELINE.
Ku Fineline Painters & Contractors, sitimangogwira ntchito; timamanga maloto anu kukhala enieni. Ntchito iliyonse imayambira pa masomphenya anu ndipo imamalizidwa ndi luso lathu, pogwiritsa ntchito zipangizo zabwino komanso akatswiri odziwa ntchito.
Kaya mukufuna kumanga nyumba yatsopano, kukonzanso yomwe ilipo, kapena, kumaliza ntchito yanu ndi finishing yapamwamba, Fineline ndiye lankho lanu.
Ntchito Zathu:
β
Kumanga Nyumba (Building Construction)
β
Building Maintenance
β
Interior Furnishings
β
Blundering
β
Ceiling & POP Installation
β
Glass & Glazing
β
Skimming
β
Plastering
β
Tiling Solutions
Timakhulupirira kuti ukatswiri umapanga kusiyana.Ndichifukwa chake timagwira ntchito mwaluso, munthawi yake, komanso mosamala kuti tikupatseni zotsatira zolimba, zokongola, komanso zokhalitsa.
CONTACT US ON:
π Tiyimbireni: +265 984 715 865
π§ [email protected]
Fineline Painters & Contractors
Precision in Every Project.