God's grace handwork

God's grace handwork Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from God's grace handwork, Carpenter, Luchenza secondary School, district thyolo, Blantyre.

23/08/2024

Follow me on WhatsApp and click the link

16/08/2024

Follow English With Abdul 👈

08/07/2024
10/03/2024



Chiopsezo, chokuti chigawo chakummwera cha dziko lino chitha kukumana ndi namondwe watsopano kuyambira mawa lino, chachepa.

Nthambi yoona za nyengo ndi kusintha kwake ndi yomwe yalengeza izi masana ano.

Akuluakulu ku nthambiyi ati kusinthaku kwadza kamba koti chiyembekezo choti dera la mpweya opepuka lomwe liri mu nyanja ya mchere ya India ukhonza kubala namondweyu chachepanso.

Mu kalata yomwe nthambiyi yatulutsa yati namondweyu sakuyembekezekanso kubadwa m'masiku atatu akudzawa.

Komabe nthambiyi yati pali kuthekera koma kochepa kuti dera la mpweya opepukawu litha kufika mdziko muno zomwe zingathandizire kusefukira kwa madzi chifukwa cha mvula yomwe ingagwe.

Madera omwe akhoza kukhuzidwa kwambiri ndi mvulayi ndi monga Nsanje, Chikwawa, Chiradzulu, Mulanje, Phalombe, Blantyre komanso Thyolo.

Wolemba: Hopecein Makhaza

Try us and you will appreciate for our hand's work.
26/01/2024

Try us and you will appreciate for our hand's work.

Address

Luchenza Secondary School, District Thyolo
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when God's grace handwork posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category