12/05/2023
Nthawi zina abale athu,azathu,maneba,akumpingo,akuchikazi komanso akuchimuna, amatha kukuikira malire pamoyo wako Ndipo safuna olo kukondwa atakuona kuti zikukuyendera.......koma ndimati Chaka Chino athu oterowo Mulungu awasiye Kakasi🙆🙆🙆🙆🙆🙆🙆....
Yehova asokoneze adani anu onse ndipo ayambe kukang'ana kuti zatheka bwanji kuti zanu ziyende????
Konzekerani kudzamvera nyimbo imeneyi yomwe mutu wake ndi MWAWASIYA KAKASI by Maggie Maggie ManganiiMaggie Manganih May, 2023.........
Ambuye akudalitseni nonse 👏