29/04/2026
Akasi mwadzuka bwa? Nkhani zabwinotu kuno ku Nyasa Food Processing Machinery and Fishery sizitha, Takubweretserani ma surface water pump ma size osiyanasiyana. Musankhe yakumtima kwanu molingana ndi kukula munda wanu komanso kuchuluka kwa madzi. Tili ndi ma pump a solar otere:
1. Pump yoyamba yomwe imafuna ma panel okwana 750w, 2 inch ndipo imapopa 15,000L pa ola (780,000 pump only)
2. Pump yachiwiri yomwe imafuna ma panel okwana 1100w, 3 inch ndipo imapopa 30,000L pa ola (989,000 pump only)
3. Pump yachitatu yomwe imafuna ma panel okwana 1500w, 3 inch ndipo imapopa 45,000L pa ola (1,480,000 pump only)
4. Pump yachinayi yomwe imafuna ma panel okwana 2200w, 4inch ndipo imapopa 60,000L pa ola (2,100,000 pump only).
Ubwino wama water pump a solar ndioti savuta kugwiritsa ntchito, Mavuto akusowa komanso kukwera mtengo kwa mafuta sakukhudzani komanso ndiolimba zedi. Chitani machawi akasi zabwinozi zisakuphonyeni.
Tipezeni lero ku Lilongwe kwa Kaphiri moyang'anizana ndi Simso oil komanso ku Area 2 -Bwalo la Njovu moyang'anizana ndi Bread Talk. Imbani phone pa nambala izi 0993176176 kapena 0993890009.