Builder Asif

Builder Asif Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Builder Asif, 6 miles, Zomba.

21/02/2026
21/02/2026
04/08/2025

DUMP PROOF COURSE PAPER. (DPC)
Musadzayesele kumanga nyumba yanu kopanda kapepela kameneka....
Ntchito yaikulu ndiyopanga separate chinyezi chomwe chimakwela chipupa Cha nyumba yanu kuchokera pansi.ambili amati kamatetezaso chiswe,izi sizoona chifukwa chiswe chimakwela ndi chipupa kuchokela pansi,angakhaleso kubokola floor yanyumba yanu,chiswe chimayenda paliponse pansi panyumbayanuyo ngati pamalopopali chiswe.

Kuthana ndi chiswe ndi nthawi imene mwakumba foundation,,gulani BIOCHRODANE,sungunulani molingana ndi ndondomeko zakagwiritsidwe tchito kake,,thilani pansi pa foundation asanayambe kumanga keneko akamanga foundation pothela pakepooo,,ikani DPC PAPER.,Akamanga khoma kumaliza,ngati mukukonzekera kupanga floor akaswa ma half anjerwa amasweledwa nkati aja,,sungunulaniso BIOCHRODANE wina thirani pansi pomwe pa sweledwa miyala paja ponse.mukatelo mwathana nalo vuto la chiswe.
Dziwani kuti ngati nyumba simuika DPC chinyezi chimakwela chipupa kupangitsa kuti paint idzikakatuka maka nthawi ya mvula,dziwaniso kuti ngati nyumbayo mwapaka lime ndipo DPC sinaikidwe lime ija imapanga inhabit ma bacteria omwe amaoletsa chipupa komanso chimamela ndele.izi zimaonekela mmanyumba ambili mukamayenda maka omwe amangidwa mmalo odikha madzi.zimapangitsaso nyumba kusweka ngati chinyezi chikukwela chipupa.
Tsatilani ndondomeko zonse zofunika pomanga kuti musadza nong'oneze Bondo.

πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό
24/07/2025

πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό

Address

6 Miles
Zomba
503

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Builder Asif posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share